FRANK Dinala GANSU

FRANK Dinala GANSU Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from FRANK Dinala GANSU, Men's clothes shop, Thyolo District Council, Blantyre.

01/06/2026



Bambo Bernado Khinda Chilichawo, a zaka 48 afa m'boma la Dowa atakomoka pa nthawi yogonana ndi chibwenzi chawo cha zaka 21, ndipo akuganiziridwa kuti anamwa chakumwa choonjezera mphamvu pogonana.

Mneneri wa Polisi ya Dowa, a Sub Inspector Alice Sitima atsimikiza za infayi, ndipo ati awiriwa anakalowa m'chipinda china pa malo ena ogona m'bomali, pomwe bamboyo anatuluka kaye kukagula mabotolo awiri a chakumwacho asanayambe kugonana.

A Sitima ati malemuyo atamwa botolo loyamba, zinthu zinayenda bwino koma atamwa botolo lachiwiri, bamboyo anakomoka mwadzidzidzi ndipo anatengeredwa ku chipatala komwe anamwalira ali mkati molandira chithandizo cha chipatala.

Zotsatira za kuchipatala zasonyeza kuti bamboyo anamwalira chifukwa cha matenda a mtima komanso kuthamanga kwa magazi komwe kukuganizilidwa kuti kunadza kaamba komwa mabotolo awiri owonjezera mphamvu.

31/05/2026

Business is business but the best business is to mind your own business 🔥🔥

30/05/2026

🌹HAPPY SABBATH 🌹

27/05/2026

L

Ogwira ntchito okwana 17 ku Moza Sweet Bakery yomwe ili pa Tsangano turn off, m'boma la Ntcheu, asonkhana ku ofesi yoona zantchito m'bomali, komwe akadandaula za nkhanza zomwe akuti akukumana nazo pomwe akugwira ntchito.

Mtsogoleri wagululi, a Bashil Douglas, awuza kuti mwini wake wa malowo, a Thokozani Erick John, amawalipira K70,000 pamwezi koma akumawachotsera malipiro ndi K10,000 kapena K20,000 akakhala kuti adwala kwatsiku limodzi, kapena kuchotsera K2,000 akawapeza akudya bread ndipo pano awachotsano ntchito.

Koma a John, poyankhura kudzera mwa a Kevin Mutoni Wakera, ati anthuwo sanachotsedwe ntchito, koma angodzichotsa okha.

Mkulu owona zantchito m'boma la Ntcheu, a Efford Geza, ati ofesi yawo inalandira dandaulolo dzulo ndipo anagwirizana ndimwini wakeyo kuti akumane naye lero koma akuti pano wakana kubwera ati chifukwa chakuti wakasuma nkhaniyi ku polisi ya Mozambique.

Wolemba: Hudson Nkumbira, Ntcheu

lGovernment has announced that the World Bank is transitioning from the current Governance to Enable Service Delivery (G...
25/05/2026

lGovernment has announced that the World Bank is transitioning from the current Governance to Enable Service Delivery (GESD) 1.0 project to a new GESD 2.0 programme, aimed at strengthening local government financing and service delivery.

The move comes as the existing GESD 1.0, a performance-based grant facility for councils, is scheduled to close on 30th June this year.

According to the spokesperson in the Ministry of Finance, Economic Planning and Decentralisation, Williams Banda, the World Bank has approved a new $80 million grant (about K140.1 billion) under GESD 2.0.

Tonic Viyuyi heads it in for Eagles to make it Eagles 1: Bullets 0
23/05/2026

Tonic Viyuyi heads it in for Eagles to make it Eagles 1: Bullets 0

Burkina Faso President Ibrahim Traore waletsa zovala za Bell/Kaunjika zochokera maiko a azungu🙌🏻Malingana ndi Traore aku...
23/05/2026

Burkina Faso President Ibrahim Traore waletsa zovala za Bell/Kaunjika zochokera maiko a azungu🙌🏻

Malingana ndi Traore akuti palibe there is no need importing clothes that people wore , got tired of it and some dumped in the Streets

Ndipo akuti waletsa zovala za kaunjikazi kulowa mdziko mwawo ngatiso njira imodzi yofuna kupanga empower ma local designers and tailors aku Burkina Faso 🇧🇫 to Patronize them and let them grow

Iye anamaliza ndikufunsa funso amvekere “munaonapo azungu ali kwao akuvala kaunjika ochokera ku Africa?”

23/05/2026

So we add chlorine in water to kill germs so that we drink dead germs 🤔

20/05/2026

Msungwana wa zaka 22, Madalo Chibwe, amene sakudziwika kwawo, wafa pozimangilira mnyumba ya wapolisi wina kwa Kamsonga mfumu yayikulu Malenga m'boma la Ntchisi.

Wofalisa nkhani za apolisi mchigawo cha pakati chaku mmawa, a Esther Mkwanda, watsimikiza za nkhaniyi, komabe wati chifukwa chenicheni chomwe chadzetsa imfayi sichikudziwika kaamba koti malemuyu sanafotokoze kalikonse mnthawi yomwe amazipha ngakhale kulemba kalata.

A Mkwanda, ati pakadali pano, sanalandire dzina la wapolisiyu ndipo apolisi akudikirabe zotsatira za chipatala kuti adziwe chomwe chadzetsa imfayi.

Koma malinga ndi yemwe watitsina khutu za nkhaniyi, awiriwa akhala ali pa ubwenzi ndipo analonjezana kuti akwatirana, koma anasemphana zochita kaamba koti wapolisiyo anatenganso mkazi wina zomwe akuganizira kuti zinakwiyitsa mtsikanayu mpaka kuzimangilira.

20/05/2026

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

Address

Thyolo District Council
Blantyre

Opening Hours

Monday 07:34 - 17:00
Tuesday 07:30 - 17:00
Wednesday 07:30 - 17:00
Thursday 07:00 - 17:00
Friday 07:00 - 17:00
Sunday 08:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when FRANK Dinala GANSU posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share