Zokonda AMAYI-hijab and casual outfits

Zokonda AMAYI-hijab and casual outfits Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zokonda AMAYI-hijab and casual outfits, Clothing (Brand), Blantyre.

Timapezeka ndi zovala za a zibambo,za chizimayi komanso za ana, kuphatikiza apo timagulisanso  nsapato ndi zikwama za m'...
20/11/2024

Timapezeka ndi zovala za a zibambo,za chizimayi komanso za ana, kuphatikiza apo timagulisanso nsapato ndi zikwama za m'manja.timaonesetsa kuti ma customer anthu tikuwasasa katundu yemwe wafika kumene pa nsika,yemwe anthu ambili akumukonda.

Timagulitsa kulikonse m'dziko la malawi ndi mayiko omwe ayandikana ndi malawi pa mitengo yosabowola nthumba

Timathanso kuwodetsa kwa omwe akufuna kuchita business pantengo owinitsa.

Mukafuna kuziwa zambili kapena ku gula(kuwoda) m***a kutilankhula ku bokosi.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zokonda AMAYI-hijab and casual outfits posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share