Dereck Grandson Chikwi JNR

Dereck Grandson Chikwi JNR ☑️ AAS STUDENT (Mr HR)
☑️ MOTIVATOR
☑️ MUSIC ARTWORK & FLIER'S
☑️ BIRTHDAY POSTER
☑️ INVITATION CARDS

Degree in Public Administration with Credit Bagged, Congratulations Franklin 🎓🔥✊
26/08/2026

Degree in Public Administration with Credit Bagged, Congratulations Franklin 🎓🔥✊

23/08/2026

Plan A Failed, Tili pa plan B

😅📍
23/08/2026

😅📍

23/08/2026

LET'S TALK ABOUT LOANS BOARDThe image reflects the pain and frustration of many students who are going to struggle and o...
22/08/2026

LET'S TALK ABOUT LOANS BOARD

The image reflects the pain and frustration of many students who are going to struggle and others ayamba kale kuvitika mene awasiyamu because of financial challenges.

You Know ine chomwe ndinaona ku Malawi kuno vuto ndi Umphawi koma Umphawi ndi Maphunziro si mzake, ngati chikusowa chakudya M'makomo what about a Student amene Ali ndi ma Assignment, ma Lab report komaso ma research?💔

Tikupempha Loans Board kuti iwonjezere chilungamo ndi kuwunika bwino ma applications onse, chifukwa ophunzira ambiri oyenerera asiyidwa popanda thandizo. Education is a right and an investment in Malawi's future, osati mwayi wa ochepa okha. No student should be forced to abandon their dreams simply because they could not access the support they deserve.
Higher Education Commission, Pakistan Tithandizen inu Chabwino ku Malawi kwatikanika😂😫💔

In this world there's only two tragedies first is not getting what you want and other one is getting it 😁 kodi inu muli ...
22/08/2026

In this world there's only two tragedies first is not getting what you want and other one is getting it 😁 kodi inu muli tragedy iti?

Munthu amene amakhala zaka 80 Ali moyo amakhala ndi pafupifupi ma second 2.5 billion m'moyo wake wonse.Kwa munthu wachic...
21/08/2026

Munthu amene amakhala zaka 80 Ali moyo amakhala ndi pafupifupi ma second 2.5 billion m'moyo wake wonse.
Kwa munthu wachichepere, chiwerengero cha masekondi otsala m'moyo wake chimakhala chocheperapo.
Mwachitsanzo, munthu wa zaka 30 amene akuyembekezeka kukhala ndi zaka zina 50 ali ndi pafupifupi masekondi 1.6 biliyoni otsala.
Chuma cha Elon Musk chikuyerekezedwa kukhala pafupifupi 866Billion (US$866 billion).

Atha kudyesa Malawi yose kwa Chaka uyu.

 Life is so much simpler when you stop explaining yourself to people and do just work for you   Morning
19/08/2026



Life is so much simpler when you stop explaining yourself to people and do just work for you

Morning

When the prophecy says, "Something BIG is coming your way," and it arrives immediately. 😂🙌
18/08/2026

When the prophecy says, "Something BIG is coming your way," and it arrives immediately. 😂🙌

Simene kulili 💔
17/08/2026

Simene kulili 💔

Address

Blantyre, Limbe
Chichiri

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dereck Grandson Chikwi JNR posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share