03/07/2026
**part 1**
*Cruuu cruu... Who's calling in the morning?? Uyu anali Piolec kudzifunsa yekha ataona k*t phone yake ikuyitana pomwe iye amagona mokwiya anadula phone ndikumapitiliza kugona...
*Cruuu cruu.... Inaliranso kachi kena monyasidwa Piolec anatenga phone ija kuyiyankha..
Hello.. Piolec anayankha
Hello... How are you doing?? Caller
Piolec.. Am doing fine how's u??
Caller.. Thanks doing well..
Piolec.. Can I know who's speaking??
*K kkkkkkk km you are serious don't you know me anayankha kwinaku akuseka.
Piolec.. Ndikufunsatu kusonyeza sindikukudziwa nde ndiyankhankhen if is possible.
Caller.. Ok by the way ndine Martha.. I hope wandidziwa..
Ohhh God... Martha iwe ulipo zoona eish unbelievable alemekezeke wa kumwamba. Anatelo Piolec modabwa km mwa chimwemwe..
*Apa Piolec anali ndi chimwemwe kwambiri pot Martha anali chibwenz chake chakale nde samakhulupilira k*t atha kudzakumananso ndi mmene anasiyanirana..
*Koma ukuoneka wachimwemwetu Piolec bwanj? Anafunsa Martha.
*Inde ndine wachimwemwe caz it seems like chinthu chomwe ndakhala ndikuchidikira chafikano. Anatero Piolec.
*Wati chinthu chomwe wakhala ukuchidikilira???? Anafunsa modabwa Martha..
Next is part 2
Osayuwara follow page share komanso comment mutiuze k*t ikunveka bwanj km muli nkhan umu