Walusungu

Walusungu We are a Home of Men's Cloth

Prisca kumene ulikoZiwa timakusowabe nyimbo zako tikadavera πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”πŸ’”πŸ’”
30/12/2025

Prisca kumene uliko
Ziwa timakusowabe nyimbo zako tikadavera πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”πŸ’”πŸ’”

Sorry 😒 koma magetsi akuyakabe😊Wina ukamachoka ku uhule uzapeza gututu wako alipakati pa Lithipe river πŸ˜‚
29/12/2025

Sorry 😒 koma magetsi akuyakabe😊

Wina ukamachoka ku uhule uzapeza gututu wako alipakati pa Lithipe river πŸ˜‚

Ku Rumphi TTC kuseli kwa mpanda munthu wazimangilira. koma sakudziwika kuti ndindani..chonde let's check ngati mwina Pal...
29/12/2025

Ku Rumphi TTC kuseli kwa mpanda munthu wazimangilira. koma sakudziwika kuti ndindani..chonde let's check ngati mwina Pali achibale a munthuyi pano....

24/12/2025

Currently situation in Mzuzu near DC office pomwe akuganizilidwa kuti waba chikwama koma sizikuziwika kuti nkati mulichan πŸ“Œ

Update -πŸ˜­πŸ’”Mtsikana tikumuonayi dzina lake ndi Janet ndipo kwawo ndi ku salima , zovesa chisoni kuti ndiamene wapangidwa ...
23/12/2025

Update -πŸ˜­πŸ’”

Mtsikana tikumuonayi dzina lake ndi Janet ndipo kwawo ndi ku salima , zovesa chisoni kuti ndiamene wapangidwa chipongwe ku phwezi mu Boma la Rumphi ndi munthu amene pakali pano sanaziwike Wamupha mwankhaza.

page ino yayankhulana ndi azizake amene amakhala nawo komaso amene amamuziwa ndipo asimikiza kuti a landrod Ake anaimbira makolo Ake amene Ali ku Salima ndipo tikunena pano anyamuka akubwera ku Rumphi kumene kuli thupi la bale wathu janet.

Thupi la Janet liri ku Montury ku chipatara chachikulu Cha Rumphi.

Janet wakhala pa Rumphi nthawi yaitali ndipo ndimunthu odziwika .

MUZIMU wake ukause mutendere πŸ’”πŸ’”πŸ˜­....

22/12/2025
Uthenga wa chisoni komaso opasa manthaπŸ˜­πŸ’”.Kukuyenda video imene kwaphedwa musikana wachichepere ku phwezi mu Boma la Rump...
22/12/2025

Uthenga wa chisoni komaso opasa manthaπŸ˜­πŸ’”.

Kukuyenda video imene kwaphedwa musikana wachichepere ku phwezi mu Boma la Rumphi. Amai amene akulongosola mu video imeneyo akuti msikanayo ndiwachilendo koma mene zikuonekela kukhala ngati wapanga nkhaza ndi mamuna amene anali naye mene akuyankhulira video imeneyo.

Chonde amene angamuzindikile akanene ku police imene alinayo pafupi.

Amene angafune kuona video imeneyi ndikuonesani popeza anena kuti munthuyo kwawo sikukuziwika and kumaloko ndi wachilendo.

Odiiii diyanike zogonela ine maloto awa andikwana nanga daily πŸ’”πŸ˜‚
22/12/2025

Odiiii diyanike zogonela ine
maloto awa andikwana nanga daily πŸ’”πŸ˜‚

Mwepan ada
21/12/2025

Mwepan ada

Address

Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Walusungu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share