Tidziwe zoona padziko lapansi

Tidziwe zoona padziko lapansi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Tidziwe zoona padziko lapansi, Women's clothes shop, Nkhotakota.

*NJIRA ZOPHERA MWAMUNA UKATOPA NAYE*```Mzimai wina atatopa nalo banja lake anafuna kungopha mwamuna wake ndipo anapita k...
03/10/2025

*NJIRA ZOPHERA MWAMUNA UKATOPA NAYE*

```Mzimai wina atatopa nalo banja lake anafuna kungopha mwamuna wake ndipo anapita kwa amayi ake kukafunsa njira imene angamuphere mwamuna wina aliyense popanda wina aliyense kuziwa kuti wachita izi ndi iye.
Ndipo atauuza amai ake anam***andiza motere, mzotheka mwana wanga zomwe ukufunazo koma, ziwa ukuenela kupanga kaye zinthu zoti anthu asakhulupilire kapena kuganiza kuti wachita ndi iwe, nde ukuenela kuchita izi

_๐Ÿ’  Uzimukonda kwambiri mwamuna wako, kuposa wina aliyense.

_๐Ÿ’ Usapange zinthu zoti m***a kuyambana nyumbamo kwa miyezi itatu.

_๐Ÿ’  Uzimuchitila nsanje kwambiri.

_๐Ÿ’  Akakupasa ndalama osamanyinyi ngakhale ili yochepa.

_๐Ÿ’  Uzimulemekeza kwambiri.

_๐Ÿ’ Usapange zinthu zomuphyesa mtima.

_๐Ÿ’  munthawi ina iliyonse mupase mwachikondi.

_๐Ÿ’ Mukamakangana chonde osamakweza mau, ndipo iwe kwako kuzikhala kupepesa basi kuopa kuti anthu angakumvereni kuti mukukangana.

_๐Ÿ’ Uzionesesa kuti mtendere ndiumene ukumanga nthenje nyumba mwako.

Ndipo mai anafunsa ukwanisa? mzima anayankha eya ama, ndipo anampasa tiufa ndipo anati uyu ndi tamerc ndipo uzithira muchakudya cha mwamuna wako daily kwa masiku makumi atatu.

Patangodusa makumi atatu mzimai uja anapitaso kwa amayi ndipo anati ama, mwamuna wanga uja wasinthiratu sindikufunanso kumupha chonde pangani zoti tarmec uja asagwirenso ntchito chonde ama, ndikamupha sindizapezanso mwamuna wabwino ngati amene uja.

Ndipo amai aja anaseka, ndipo anati:

kkkkkkk kuterokotu ufa uja sanali tarmec ayi, unali ufa chabe
chimene chimasowekela mwa iwe anali malangizo amene ndinakupasa aja, waona? Mwamunayotu sanasinthe ayi ndi yemwe uja... koma iwe ukumuona kusintha chifukwa iwe mwini wasintha chikhalidwe, mwana wanga banja ndi chikhalidwe, chikhalidwe mchomwe chimapangisa kuti banja likhale lokoma.

Kuyambira lero uzisatila malangizo amene ndakupasa kuti banja likhale lolongosoka```
๐Ÿ‘ซ๐Ÿพ
Mulungu akudalitseni

23/09/2025

Pomwe a Malawi akuyembekezera kumva zotsatira zomaliza zotsimikizika za Chisakho chapatatu chatsogoleri wa dziko, aphungu ndi makhansala kuchokera ku bungwe la MEC, maonekedwe a chipinda chomwe chikugwilitsidwa ntchito polengeza zotsatira zachisakhozi chasitha maonekedwe pomwe kwaikidwa mipando yooneka bwino kwambiri kutsogolo komwe kumakhala adindo

Kodi kugwanji lero?

(Wolemba Emmanuel Chiocha)

03/09/2025

USA - China Tensions

India ikuzunguza kwambiri anthu akulephera kuimvesa kuti imaganiza bwanji .

Prime Minister wa India anapita Ku China kukakhala nao pa ceremony ya China Military parade . Kumeneko Russia President Putin ndi President Wa North Korea Kim anali komweko. Anthuwa anagwirizana mfundo ya umodzi . Kutetezana , Kupanga business limodzi komanso Kulimbana ndi ulamulilo wa chi America pa malonda and security

Dzulo USA yayamba Training ya Nkhondo Ku Australia ndipo India yapezeka kuti yajoina ikupanga Nao training pamodzi ndipo ikuyamikila ukadaulo wa USA . India yanena kuti ilimbikisa Ubale wabwino ndi USA pankhani ya chitetezo, Malonda ndi Kulimbana ndi ulamulilo wa nkhaza wa maiko ena

๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…Mwenye ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™

Today's news 1. Oimila DPP ngati commissioner Ku MEC Katswiri wa ma computer amukananso. Uyu ndi wachitatu kukanidwa . D...
03/09/2025

Today's news

1. Oimila DPP ngati commissioner Ku MEC Katswiri wa ma computer amukananso. Uyu ndi wachitatu kukanidwa . DPP imangopereka akatswiri ama computer okha okha kuti awaimilile onsewo akukanidwabe.

2. Boma likubwereka kwambiri ndalama zoyendesera Dziko lino makamaka kuyambila mwezi wa July mpaka Pano . Kubwereka mpaka 100%

Ministry of Trade  & CFTCAkulu Akulu a Boma nthambi ya Trade kuzela Ku Bungwe la CFTC apereka chipepala Ku company ya Ag...
02/09/2025

Ministry of Trade & CFTC

Akulu Akulu a Boma nthambi ya Trade kuzela Ku Bungwe la CFTC apereka chipepala Ku company ya Agrycom kuti ifotokoze zifukwa ikusungula matumba a cement Ku warehouse Yake. Company yati iyankha .

Iwo ati company iyi ndi imodzi mwa iyo inalandila Nao ndalama Ku Boma ( Forex ) kugula cement Ku Zambia wa 26 pin

Let me Congratulate and appreciate this mature way of handling Business issues . This is the best way we engage Traders osati ma camera kumawashatapula ngati ana . Embarrassing them publicly.Zimakoleza Moto unnecessarily.

Special thanks to the PS Madam Zakeyo. That's maturity, Professionalism and Official way of managing Business affairs

Looking forward kumva Ku company akayankha

02/09/2025

Sudan landslide

Pakanali Pano Phiri lalikulu Ku Dafur Ku Sudan kumalo komweko laphulika ndipo Mazi ochuluka apanga Msinje wanyuwani kudusa kumene mizi ya anthu inali

Zimiyala zikulu zikulu zikutsika Ku Phiri nkumasinja anthu.

Kwinaku ntchito yotola matupi a anthu oposa 1 sauzande amwalila Ili mkati

Sudan yapempha United Nations kuti ithamange athandize

Will drop videos soon after verification

01/09/2025

News
Ku Ntchisi A Chalekana Achotsa Moyo wa a Thokozani. Maliro Ali mkati Moika

Nkhani yake ndi yoti a Chalekana anapeleka ganyu kwa A Thokozani youmba Njerwa .

Kenako Patatha masiku anabwera kuzayendera ntchito koma sanasangalale kuti ntchito imachedwa . Njerwa amaganizila Iwowo kuchuluka Kwake zinali zochepela ndi zimene a Thokozani Anaumba. Izi zinawanyasa a Chalekana kenako anangoganiza zoti ameneyu asakhalenso ndi Moyo asavote nao ndipo anakhapa a Thokozani nkufera pomwepo Iwo nkuthawa.

Uthenga utafika kumudzi azibale a Thokozani Anayamba kutentha nyumba zonse za a Chalekana kenako Apita kukatenthanso nyumba zonse za abale a Chalekana ngakhale sizinawakhuze , Anyamukanso kukatentha nyumba zonse za anzao a Chalekana chifukwa cholusa ....panopa akufuna atenthe nyumba ya aliyense ofanana maonekedwe ndi a Chalekana komanso aliyense amene Ali ndi Dzina lofanana ndi Chalekana

Nkhani Ili Ku Police

Ku USA bambo wina, Jorge Fernandez akusumila clinic yotchedwa A&E Med Spa.Mkazi wa Jorge anamuwuza Jorge kuti akufuna ak...
22/08/2025

Ku USA bambo wina, Jorge Fernandez akusumila clinic yotchedwa A&E Med Spa.

Mkazi wa Jorge anamuwuza Jorge kuti akufuna akapangitse surgery yokulitsa mbina (BBL - Brazilian Butt Lift).
Akuti Jorge anamuwuza mkazacheyo kuti palibe chifukwa chopangila izi chifukwa amamukonda iye mmene aliri.

Koma madam a Jorge anati akufunitsitsa kukuza mbina. Anapanga book appointment ku A&E Med Spa ndipo anapita ku operation.

Pa operation, amachotsa mafuta pamalo pamene alipo ambiri, nkuwapopera mu mbinamo. Choncho zimangokhala ngati thako lanenepa komanso amalipanga shape.

Madam a Jorge anapanga suffer pulmonary embolism nkukomoka.

BBL ndi imodzi mwa ma surgery owopsya pa dziko lapansi. Akamapopera fat mu mbinamo, amayenera kuwonetsetsa kuti asasokoneze nkupopera mu ntsempha.

Pulmonary embolism - anayika fat mu mtsempha wopititsa magazi mu mtima.

Madam a Jorge akudyestedwa ndi tube, sadzayendanso ndipo sadzalankhulanso.

  front page: Economic, good governance and social service provision issues dominated discussions during the debate whic...
22/08/2025

front page: Economic, good governance and social service provision issues dominated discussions during the debate which the Presidential Debate Taskforce organised in Lilongwe last evening.

https://times.mw/etimes/

21/08/2025

Follow My page zambili zisakuphonyen

Address

Nkhotakota

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tidziwe zoona padziko lapansi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share