Kuseka ndi. Kuphunzila

Kuseka        ndi.   Kuphunzila Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kuseka ndi. Kuphunzila, Men's clothes shop, Blantyre.

koma kwavuta
04/01/2026

koma kwavuta

oyimba wathu uyuuuuuuu
27/12/2025

oyimba wathu uyuuuuuuu

13/12/2025
30/11/2025

🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬
NDINZANGA
part 1
🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬🎬

ka story kanyamata wina ndintsika wina tiyeni tiwone k*t muli zotani
πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½πŸ“½

linali loweluka pamene jonh amasowazochita anagniza zopita kokayenda kwinako akufuna k*tayisa nthawi ananyamuka ulendo wake alinkati moyenda amawona ntsika wina ak*tuluka kumpanda naye akupita komwe amalowera jonh. apa jonh sanaphweketse koma kumuthamangila nkazi uja atamuyandikula anamuyankhala

πŸ‘¦πŸ”Šase
πŸ‘§πŸ”Šine?
πŸ‘¦πŸ”Šeya bho
πŸ‘§πŸ”Šbho
πŸ‘¦πŸ”Šndakuwona ukuchokela kumpanda uwo umakhala kumene?
πŸ‘§πŸ”Šeya
πŸ‘¦πŸ”Šoky nde uku ukupita k*ti?
πŸ‘§πŸ”Špalibe ndikungofuna kupitidwako mphepozina kumpandako kwandikwana
πŸ‘¦πŸ”Šbwanji umakhalako wekha?
πŸ‘§πŸ”Šeya
πŸ‘¦πŸ”Šmakolo ako bwanji kapena azibale ako
πŸ‘§πŸ”Šndimakhala ndi bambo anga kwathu tiliko ana awili ine ndiwo maliza woyambayo ali ku school ku U.K. nde bambo anga amakhala kuntchito tsiku lonse nde ndimangokhalako ndekha ndekha
πŸ‘¦πŸ”Šnde zosangalasatu
πŸ‘§πŸ”Šnde iweyo umakhala k*ti?
πŸ‘¦πŸ”Škubangwe
πŸ‘§πŸ”Šmmmmmm kwa anthu okuba kuja
πŸ‘¦πŸ”Šanakunamiza ndindani?
πŸ‘§πŸ”Šaaaaa kumanveka choncho
πŸ‘¦πŸ”Šosamakhulupilila zinthu zimene sunawonepo
πŸ‘§πŸ”Šoky ndakunva apapa ndibwelelep***a cause adadi azitulukila p***ano
πŸ‘¦πŸ”Šokay nane ndibwelelenso p***a koma ndakudyadila
πŸ‘§πŸ”Šoky

John anasiyana naye ntsikana uja

TIYENI TIPITE KU PART 2 TINVE K*T KULI ZOTANI
OSAYIWALA KUPANGA FOLLOW NDI LIKE K*TI TINKHANITI TIZIKUPEZANI MOSAVUTA NGATI TIKUSANGALASA PANGAN COMMENT K*TI NDIZIPITILIZA
ZIKOMπŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™πŸ™

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kuseka ndi. Kuphunzila posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share