Ka sir Gaza artist Music

Ka sir Gaza artist Music J

14/11/2021

NAMADINGO WACHITA NGOZI

Oyimba odziwika bwino muno m'Malawi, Patience Namadingo adachita ngozi dzulo pa 13 November ku Chigumula, Blantyre.

Malingana ndi Kafukufuku wathu panthawiyi oyimbayu adali kuyendela galimoto ya ntundu wa (Mercedes Benz) ndipo atafika malo ena ku Chigumulako iye adalephera kuongolera bwino mpaka galeta lakeli lidalowa kuphompho.

Atafunsidwapo za Nkhaniyi, Dr Namadingo adanenena mophiphiritsa kuti " Galimoto yachita ngozi Ndiyangadi, Koma ine sindidali Mkatimo"

Ndipo nkhani yosangalatsa ndiyokuti Dr Namadingo sadavulare pa Ngoziyi.

-Naomi Kamiza




01/03/2021

NDIKHALA NDKUTULITSA TRACK WASOPANO MUTU WAKE KUTCHUKA ANDI πŸ•™. πŸ“’πŸŽ§πŸŽ§ &πŸ“ΊπŸ“Ί. πŸ’―πŸ’―πŸ’―βœ…βœ…πŸ’«. πŸ’―πŸ’―πŸ’― 0:0 βͺ β–Ά ⏩ 3:25
________________________________

29/01/2021

Address

Www Ka Sir Gaza. Com
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ka sir Gaza artist Music posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share