Mtundu Brands

Mtundu Brands Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mtundu Brands, Clothing (Brand), Lilongwe.

We promote Malawian cultures through branding on various merchandise including mugs, bottles, hoodies, t-shirts, golfshirts, hats, caps, pens, banners, fisherman's jackets

18/04/2026

Screenprinting?
0884919726

20/03/2026
Aaah! Fadah...Mufuna ma   a quality a ku conference, kukongoletsa mu nyumba kapena ofesi?Mwapanga ukwati kapena kuti mul...
16/02/2026

Aaah! Fadah...Mufuna ma a quality a ku conference, kukongoletsa mu nyumba kapena ofesi?

Mwapanga ukwati kapena kuti muli ndi chibwenzi cha pa mtima chokapitilira ku banja ndipo mufuna mphatso yomveka bwino komanso yokhalitsa ngati chikumbutsiro? Nanga birthday present kuchita kusauka nayo maganizo fadah? prints bwa? Kapena architectural design prints?

Kapena mungofuna chi calendar chachikulu bwino inu makolo mwatopa nkufunsa ma date kwa neba?

Bwelani Ku , Office No. 2 ku 6 Miles pa Engen Filling Station (ya blue) ku kungodutsa Police Road Block mukamapita ku Blantyre.

Mukafuna picture framing services for your treasured memories zimathekanso.

Call or WhatsApp us today at 0884919726,

Embroidery ya ma uniform a ana, nurses, office wear, work suits, ngakhalenso pa nsapato? Timayika ma logo a quality osat...
06/02/2026

Embroidery ya ma uniform a ana, nurses, office wear, work suits, ngakhalenso pa nsapato? Timayika ma logo a quality osati zongobhakasha-bhakasha ngati ma telala osoka zigamba a ma 90s.

Ma logo pa zipewa, ma shirt, uniforms, name tags ana asamawabele uniform ku school. We also print ma banner, ma stickers, vehicle branding, signposts, ma mug, printing ID cards ndi zina zambiri.

Mtundu Brands is your ultimate go-to guru for from only MWK3000. Hit us up or WhatsApp 0884919726 musiyanitse ndi ajawa. Kutali timatumizanso!!!!

Tikupezeka ku Lilongwe pa 6 Miles, Engen Filling Station after Police Roadblock mukamapita ku Blantyre.

Quality embroidery? Wegot you
02/02/2026

Quality embroidery? Wegot you

Get embroidery needs? We got you

27/01/2026
27/01/2026

Address

Lilongwe
207222

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mtundu Brands posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mtundu Brands:

Share