Van Victor

Van Victor Gospel Musician πŸŽΆπŸ“ŒπŸ–‡οΈπŸ”₯

Any Business +265884083263

Based In Ntcheu πŸ€™
(1)

21/08/2026

Arsenal 3:0 inayo
Good night

21/08/2026

Ndiyamike kwabasi kwanonse amene munandigayira ndlama ndipo ndalandila
Mulungu akudalitseni πŸ™

21/08/2026

Dear Aguru ✍️

Choyamba mulibwanji? ngati muli bwino ndiyamike kwabasi 🀝

ine ndi Van Victor Gospel artist ndimayimba nyimbo za Uzimu βœ‹

Ndimafunaso ndipereke ulemu kwamene muli pa page pano makamaka amene manditsata komaso kundimvetsetsa ndikuti zikomo πŸ™Œ

Komaso ndiyamike kwabasi amene mumatsata ndi kumvetsetsa label Yanga ya (The God instruments)

Chifukwa mu label imeneyi muli zambili Monga

(1) Kupanga umodzi Ngati ana amayi modzi
(2) Kutukulana Umoyo wa Uzimu
(3) Kuthandizana munjira za mbili...etc

ndi chifukwa amene amandimvetsa chimene ndili sakhumudwa nane komaso ndinapereka mtima wanga Kwa munthu aliyese pano Ngati m'bale wanga 🀝

Page ino sitipereka chinthandizo Kwa munthu ndi njira yakuti tipeze ma followers kapena ma like ayi βœ‹ ndie we are family Aguru 🀝

21/08/2026

Anja mumafuna mundigayire ndlama Anja number ndi iyiii πŸ‘‡
0993 27 83 34
thanks for your loveπŸ›οΈπŸ€

21/08/2026

Ndlama kumapatsana Aguru ,naneso ndigaireni ya FantaπŸ›οΈπŸ«£

21/08/2026

Money laundering
Ka English aka asaa!! 😎

21/08/2026

Chimwemwe chidza Ku m'mawa tamuwuzeni Father Jesus akuze malire anu pa chilichonse chimene mukusaka tsiku lalero βœ‹

20/08/2026

Good night

20/08/2026

Tamasapotani Artist wanu inu aaaah! Aguru anji

Address

Lilongwe

Telephone

+265888121268

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Van Victor posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Van Victor:

Shortcuts

Share