TM Bello Drips Shop

Directions

TM Bello Drips Shop We sell all types of Clothes. We are in Lilongwe at Nathenje Depot near Roadblock. closed yet..we will let you to know when it will opened again.

Thanks 🤝

(CLOSED YET🚪)

16/04/2025

Funso kwa Anyamata okhaokha;

"Anapanga chani kuti mudziwe zoti Mkazi ameneyu sakuyenela inuyo ndipo munamusiya?"

16/04/2025

Tafika 1K nde popanga congratulate tufuna tigawe ma Units kwa anthu 5 koma sititchula figure titchula Munthu akawina. Pangani invite anzanu okwana 5 okha kuti apange like page ino ndipo akapanga accept mwawina. Tumizani screenshot yanu ku inbox kwathu olo pa Whatsapp 🤝

Send a message to learn more

Rating WADONGO by Jay Jay Cee Mw and MAN CHI chiwamboNyimbo sizodabwitsa kuiona isakuchita bwino interms of Views komans...
21/03/2025

Rating WADONGO by Jay Jay Cee Mw and MAN CHI chiwambo

Nyimbo sizodabwitsa kuiona isakuchita bwino interms of Views komanso kukambidwakambidwa as sign yoti anthu ailandila

1 Jay Jay Cee should switch his style. There is no way munthu wankulu pa music ngati Iyeuja asamaonese progress Zaka zonsezi. Nyimbo iliyose ya JJC kaimbidwe kake kamakhala komwekomweko of course is his identity komabe should at least switch his flows and lyrics tisamachite kumuziwilatu zomwe abwele nazo. He should be unpredictable

2 Nyimbo ija ma Verse ndi Hook komanso Title zikusiyana. Title ikufanana ndi Hook koma ma Verse anenedwamo Zina differently to Concept. I think concept was about akazi ndi amuna onse ndichimozimodzi bola kungoumba WADONGO and ukavela Hook ikugwilizanadi ndi title komano Content Yama Verse ndiina. Verse ya JJC ikukamba zokhala ngati akulangiza munthu kuti alimbikile school zomwe it's pallarel to Concept yanyimbo komanso Hook. Nayeso man-chi walowa zosiyana wabwela ndiinayake yosiyana ndizosezo osaziwikaso kuti akukamba ziti pena ukamuva ngati akumuuza nkazi kuti akungomusiya sangamudandaule and so on zomwe nkumbali kwambiri kwa Concept

3 beat selection yavuta koopsa. Ma beat a JJC is always same ayese kumapangisako enaake osakhala auchi JJC eh! No. Zimenezija tinavela zinatikwana and game inasintha we must see a little progress in him there is no way munthu ungamangoimba zofanana kuchokela 2018 mpaka lero ma beat kumangoveka same mwina amapanga yekha komano it's trash

All in all Nyimboyi ndikuipasa -1 pa 10 because there is no any creativity in that.👎🗑️🚮

Tomorrow we are rating Ndabweraso Remix of MarMartin AngelesIKKIKKMfuMfumu HyphenBarBarry Uno@Base Cube and so on

Address

Nathenje

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when TM Bello Drips Shop posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category