Faluku

Faluku Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Faluku, Midrand.

Rapper who died of drag ods
27/01/2026

Rapper who died of drag ods

Pamene Boma la China layamba kufufuza Mkulu wao wa Asilikali pa Mlandu ogulitsa information ya Military Ku USA , mphekes...
26/01/2026

Pamene Boma la China layamba kufufuza Mkulu wao wa Asilikali pa Mlandu ogulitsa information ya Military Ku USA , mphekesela zayamba kumveka kuti Asilikaliwa alipo angapo amene akuganizilidwa kuti afuna kulanda Boma ndi kugwetsa president

16/01/2026

“Nkhani Ya Bambo Waku Mchinji Ine Lawyer Sylvester Ayuba Ndimuyimira Ulere Ndiosalakwa”

-Khoti la a Magistrate ku Mchinji lapeza Ernest Chimpeni wazaka 37 ndi mlandu wogwirira mwana atasimikiza kuti mtsikanayo anali wosakwana zaka 18, ngakhale iye atanena kuti ali ndi zaka 19 komanso kuwonetsa chiphaso cha mzika cha dziko chomwe chimanena kuti anabadwa mu 2006.

Khoti linamva kuti Chimpeni anayamba zokonzekera ukwati ndi banja la mtsikanayo ndipo anapereka K30,000 ndi nkhuku ngati gawo la mwambo wa malowolo, koma pambuyo pake anazindikira kuti mtsikanayo anali ndi pakati pa mwamuna wina kenaka anapita kwawo kwa makolo kuti amubwenzere ndalama ndi nkhuku za banja zisapitilirenso zomwe zinachititsa makolo ake kukatokoza nkhaniyi kwa apolisi.

A Magistrate Godfrey Nyirenda anagamula kuti pansi pa kusintha kwa Penal Code ka 2023, kukhulupirira kuti mtsikana siwamkulu potengera chilungamo choti anabadwa 2008 osati 2006 ndipo pali mulandu okuti ayankhe posatengera chiphatso chauzika popeza mwanayo ananama zaka chabe Cholinga athe kuvota Chaka chatha.

Chimpeni akusungidwa m’ndende akuyembekezera chilango Lolemba likudzali.

Pankhaniyi lawyer Ayuba wazipeleka kukayimira bambo omangidwayu pa court mwa ulere.

Address

Midrand

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Faluku posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share